A Malawi ambiri akunyerabe ku tchire (malawi24.com)

Ngakhale m'madera ambiri muli zikwangwani zoti “tidasiya kunyera ku tchire,” zadziwika kuti iri ndi bodza lankunkhuniza chabe pomwe lipoti latsindika kuti anthu ambiri alibe zimbudzi ndi zipangizo zina za ukhondo.Izi zadziwika Lachisanu pa mwambo wotsegulira Presidential Compact on Water, Sanitation and Hygiene (WASH), komwe Wachiwiri kwa Nduna ya Zaumoyo ndi Ukhondo, Charles Chilambula, adati dziko...

A Malawi ambiri akunyerabe ku tchire Ngakhale m'madera ambiri muli zikwangwani zoti “tidasiya kunyera ku tchire,” zadziwika kuti iri ndi bodza lankunkhuniza chabe pomwe lipoti latsindika kuti anthu ambiri alibe zimbudzi ndi... https://malawi24.com/2026/08/15/a-malawi-ambiri-akunyerabe-ku-tchire/

0 comments — live from bluesky

No comments yet.